Deuteronomo 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a chilamulo ichi, kutinso azitsatira malangizo ake.+ Salimo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+ 1 Timoteyo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sinkhasinkha zinthu zimenezi mozama.+ Dzipereke pa zinthu zimenezi kuti anthu onse aone kuti ukupita patsogolo.+ Yakobo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma woyang’anitsitsa m’lamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu, amene amalimbikira kutero, adzakhala wosangalala+ polichita chifukwa chakuti sali wongomva n’kuiwala, koma wochita.+
19 “Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a chilamulo ichi, kutinso azitsatira malangizo ake.+
2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+
15 Sinkhasinkha zinthu zimenezi mozama.+ Dzipereke pa zinthu zimenezi kuti anthu onse aone kuti ukupita patsogolo.+
25 Koma woyang’anitsitsa m’lamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu, amene amalimbikira kutero, adzakhala wosangalala+ polichita chifukwa chakuti sali wongomva n’kuiwala, koma wochita.+