Yoswa 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Buku la malamulo ili lisachoke pakamwa pako,+ uziliwerenga ndi kusinkhasinkha usana ndi usiku, kuti uonetsetse kuti ukutsatira zonse zolembedwamo.+ Pakuti ukatero, udzakhala ndi moyo wopambana, ndipo udzachita zinthu mwanzeru.+ Salimo 35:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Lilime langa linene chapansipansi za chilungamo chanu,+Ndipo likutamandeni tsiku lonse.+ Salimo 119:97 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Ndimakonda kwambiri chilamulo chanu!+Ndimasinkhasinkha chilamulocho tsiku lonse.+ 1 Timoteyo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sinkhasinkha zinthu zimenezi mozama.+ Dzipereke pa zinthu zimenezi kuti anthu onse aone kuti ukupita patsogolo.+
8 Buku la malamulo ili lisachoke pakamwa pako,+ uziliwerenga ndi kusinkhasinkha usana ndi usiku, kuti uonetsetse kuti ukutsatira zonse zolembedwamo.+ Pakuti ukatero, udzakhala ndi moyo wopambana, ndipo udzachita zinthu mwanzeru.+
15 Sinkhasinkha zinthu zimenezi mozama.+ Dzipereke pa zinthu zimenezi kuti anthu onse aone kuti ukupita patsogolo.+