Salimo 71:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhalenso lilime langa lidzalankhula chapansipansi za chilungamo chanu tsiku lonse,+Pakuti ofunafuna kundigwetsera tsoka achita manyazi ndipo athedwa nzeru.+ Salimo 145:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakutamandani tsiku lonse.+Ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
24 Ngakhalenso lilime langa lidzalankhula chapansipansi za chilungamo chanu tsiku lonse,+Pakuti ofunafuna kundigwetsera tsoka achita manyazi ndipo athedwa nzeru.+