Salimo 35:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+ Salimo 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+ Salimo 71:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu otsutsana nane achite manyazi, iwo awonongedwe.+Amene akufunafuna kundigwetsera tsoka adziphimbe ndi chitonzo ndiponso manyazi.+
26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+
14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+
13 Anthu otsutsana nane achite manyazi, iwo awonongedwe.+Amene akufunafuna kundigwetsera tsoka adziphimbe ndi chitonzo ndiponso manyazi.+