Yohane 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+
20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+