Mateyu 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, iwo anachoka mwamsanga pamanda achikumbutsowo, ali ndi mantha ndiponso chimwemwe chochuluka, ndipo anathamanga kukauza ophunzira ake.+ Luka 24:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma iwo, pokhalabe osakhulupirira+ chifukwa cha chimwemwe ndi kudabwa, iye anawafunsa kuti: “Kodi muli ndi chakudya chilichonse pano?”+ Yohane 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atanena zimenezi, anawaonetsa manja ake ndi pambali pa mimba paja.+ Pamenepo ophunzirawo anasangalala+ poona Ambuyewo.
8 Choncho, iwo anachoka mwamsanga pamanda achikumbutsowo, ali ndi mantha ndiponso chimwemwe chochuluka, ndipo anathamanga kukauza ophunzira ake.+
41 Koma iwo, pokhalabe osakhulupirira+ chifukwa cha chimwemwe ndi kudabwa, iye anawafunsa kuti: “Kodi muli ndi chakudya chilichonse pano?”+
20 Atanena zimenezi, anawaonetsa manja ake ndi pambali pa mimba paja.+ Pamenepo ophunzirawo anasangalala+ poona Ambuyewo.