Yohane 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma mmodzi wa asilikaliwo anamulasa ndi mkondo m’mbalimu cham’mimba,+ ndipo nthawi yomweyo panatuluka magazi ndi madzi. 1 Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+
34 Koma mmodzi wa asilikaliwo anamulasa ndi mkondo m’mbalimu cham’mimba,+ ndipo nthawi yomweyo panatuluka magazi ndi madzi.
1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+