Yohane 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo unakhalapo kudzera mwa iye,+ ndipo moyowo unali kuwala+ kounikira anthu. Yohane 6:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Simoni Petulo+ anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu amoyo wosatha.+
68 Simoni Petulo+ anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu amoyo wosatha.+