Yohane 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti monga Atate ali nawo moyo mwa iwo wokha,+ alolanso Mwana kukhala nawo moyo mwa iye yekha.+ Machitidwe 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+ 1 Yohane 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+ 1 Yohane 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Umboni umene waperekedwa ndi wakuti, Mulungu anatipatsa moyo wosatha,+ ndipo tinaulandira kudzera mwa Mwana wake.+
15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+
2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+
11 Umboni umene waperekedwa ndi wakuti, Mulungu anatipatsa moyo wosatha,+ ndipo tinaulandira kudzera mwa Mwana wake.+