Yohane 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Wophunzira ameneyu+ ndiye akuchitira umboni zinthu zimenezi. Iyeyu ndi amenenso analemba zinthu zimenezi, ndipo tikudziwa kuti umboni umene akupereka ndi woona.+ Machitidwe 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yesu ameneyo Mulungu anamuukitsa, ndipo tonsefe ndife mboni za choonadi chimenecho.+
24 Wophunzira ameneyu+ ndiye akuchitira umboni zinthu zimenezi. Iyeyu ndi amenenso analemba zinthu zimenezi, ndipo tikudziwa kuti umboni umene akupereka ndi woona.+