Yohane 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu amene anaona zimenezo akuchitira umboni, ndipo umboni wakewo ndi woona. Munthu ameneyu akudziwa kuti amanena zoona, kuti inunso mukhulupirire.+ 3 Yohane 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu onse amuchitira umboni Demetiriyo.+ Choonadinso chikumuchitira umboni. Ifenso tikuchitira umboni,+ ndipo iwenso ukudziwa kuti umboni umene timapereka ndi woona.+
35 Munthu amene anaona zimenezo akuchitira umboni, ndipo umboni wakewo ndi woona. Munthu ameneyu akudziwa kuti amanena zoona, kuti inunso mukhulupirire.+
12 Anthu onse amuchitira umboni Demetiriyo.+ Choonadinso chikumuchitira umboni. Ifenso tikuchitira umboni,+ ndipo iwenso ukudziwa kuti umboni umene timapereka ndi woona.+