Yohane 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma izi zalembedwa+ kuti mukhulupirire kuti Yesu alidi Khristu Mwana wa Mulungu, ndi kutinso, mwa kukhulupirira,+ mukhale ndi moyo m’dzina lake. Yohane 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Wophunzira ameneyu+ ndiye akuchitira umboni zinthu zimenezi. Iyeyu ndi amenenso analemba zinthu zimenezi, ndipo tikudziwa kuti umboni umene akupereka ndi woona.+ 1 Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+
31 Koma izi zalembedwa+ kuti mukhulupirire kuti Yesu alidi Khristu Mwana wa Mulungu, ndi kutinso, mwa kukhulupirira,+ mukhale ndi moyo m’dzina lake.
24 Wophunzira ameneyu+ ndiye akuchitira umboni zinthu zimenezi. Iyeyu ndi amenenso analemba zinthu zimenezi, ndipo tikudziwa kuti umboni umene akupereka ndi woona.+
1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+