Yohane 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti aliyense wokhulupirira iye akhale nawo moyo wosatha.+ Yohane 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+ 1 Petulo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 popeza ndinu otsimikiza kuti chikhulupiriro chanu chidzachititsa kuti miyoyo yanu ipulumuke.+ 1 Yohane 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikukulemberani izi kuti mudziwe kuti inu amene mumakhulupirira m’dzina la Mwana wa Mulungu+ muli ndi moyo wosatha.+
24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+
13 Ndikukulemberani izi kuti mudziwe kuti inu amene mumakhulupirira m’dzina la Mwana wa Mulungu+ muli ndi moyo wosatha.+