Yohane 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Iye wokhulupirira+ mwa Mwanayo ali nawo moyo wosatha.+ Wosamvera Mwanayo sadzauona moyowu,+ koma mkwiyo wa Mulungu ukhalabe pa iye.+ Yohane 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma izi zalembedwa+ kuti mukhulupirire kuti Yesu alidi Khristu Mwana wa Mulungu, ndi kutinso, mwa kukhulupirira,+ mukhale ndi moyo m’dzina lake.
36 Iye wokhulupirira+ mwa Mwanayo ali nawo moyo wosatha.+ Wosamvera Mwanayo sadzauona moyowu,+ koma mkwiyo wa Mulungu ukhalabe pa iye.+
31 Koma izi zalembedwa+ kuti mukhulupirire kuti Yesu alidi Khristu Mwana wa Mulungu, ndi kutinso, mwa kukhulupirira,+ mukhale ndi moyo m’dzina lake.