Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+ Yohane 6:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndithudi ndikukuuzani, Wokhulupirira ali nawo moyo wosatha.+ Aheberi 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo atakhala wangwiro,+ anakhala ndi udindo wopereka chipulumutso chamuyaya+ kwa onse omumvera,+
16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+