Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 45:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa chifukwa chokhala pa mgwirizano ndi Yehova+ ndipo adzakhala wopulumutsidwa mpaka kalekale.+ Anthu inu simudzachita manyazi+ ndipo simudzanyozeka+ mpaka kalekale, ngakhale kwamuyaya.

  • Yesaya 49:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno iye anati: “Si nkhani yochepa kuti iweyo wakhala mtumiki wanga, n’cholinga choti ubwezeretse mafuko a Yakobo ndi kubweza Aisiraeli amene ali otetezeka.+ Ndakupereka kuti ukhale kuwala kwa mitundu ya anthu,+ kuti chipulumutso changa chifike mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+

  • Yesaya 53:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino+ ndipo adzakhutira.+ Chifukwa cha zimene akudziwa, mtumiki wanga wolungamayo+ adzachititsa kuti anthu ambiri azionedwa olungama,+ ndipo adzasenza zolakwa zawo.+

  • Luka 1:69
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 69 Iye watikwezera ife nyanga*+ yachipulumutso m’nyumba ya mtumiki wake Davide,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena