Yesaya 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ineyo Yehova pochita zinthu mwachilungamo, ndinakuitana+ ndipo ndinakugwira dzanja.+ Ndidzakuteteza ndiponso ndidzakupereka monga pangano kwa anthu+ ngati kuwala kwa mitundu ya anthu,+ Mateyu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga,+ amene moyo wanga ukukondwera naye. Ndidzaika mzimu wanga pa iye,+ ndipo adzasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni kwa anthu a mitundu ina. Luka 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.” Machitidwe 13:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipotu Yehova anatiikira lamulo lakuti, ‘Ndakuikani monga kuwala kwa anthu a mitundu ina,+ kuti mukhale chipulumutso mpaka kumalekezero a dziko lapansi.’”+
6 “Ineyo Yehova pochita zinthu mwachilungamo, ndinakuitana+ ndipo ndinakugwira dzanja.+ Ndidzakuteteza ndiponso ndidzakupereka monga pangano kwa anthu+ ngati kuwala kwa mitundu ya anthu,+
18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga,+ amene moyo wanga ukukondwera naye. Ndidzaika mzimu wanga pa iye,+ ndipo adzasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni kwa anthu a mitundu ina.
32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.”
47 Ndipotu Yehova anatiikira lamulo lakuti, ‘Ndakuikani monga kuwala kwa anthu a mitundu ina,+ kuti mukhale chipulumutso mpaka kumalekezero a dziko lapansi.’”+