Yesaya 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ine, Yehova Mulungu wako, ndagwira dzanja lako lamanja.+ Ine amene ndikukuuza kuti, ‘Usachite mantha.+ Ineyo ndikuthandiza.’+
13 Pakuti ine, Yehova Mulungu wako, ndagwira dzanja lako lamanja.+ Ine amene ndikukuuza kuti, ‘Usachite mantha.+ Ineyo ndikuthandiza.’+