Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 11:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 M’tsiku limenelo,+ padzakhala muzu wa Jese+ womwe udzaimirire ngati chizindikiro kwa anthu.+ Ngakhale anthu a mitundu ina adzatembenukira kwa iye kuti awatsogolere,+ ndipo malo ake okhalapo adzakhala aulemerero.+

  • Yesaya 42:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Ineyo Yehova pochita zinthu mwachilungamo, ndinakuitana+ ndipo ndinakugwira dzanja.+ Ndidzakuteteza ndiponso ndidzakupereka monga pangano kwa anthu+ ngati kuwala kwa mitundu ya anthu,+

  • Yesaya 49:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno iye anati: “Si nkhani yochepa kuti iweyo wakhala mtumiki wanga, n’cholinga choti ubwezeretse mafuko a Yakobo ndi kubweza Aisiraeli amene ali otetezeka.+ Ndakupereka kuti ukhale kuwala kwa mitundu ya anthu,+ kuti chipulumutso changa chifike mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+

  • Machitidwe 13:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Ndipotu Yehova anatiikira lamulo lakuti, ‘Ndakuikani monga kuwala kwa anthu a mitundu ina,+ kuti mukhale chipulumutso mpaka kumalekezero a dziko lapansi.’”+

  • Machitidwe 26:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Zolembazo zinaneneratu kuti Khristu adzavutika,+ ndipo monga woyamba kuukitsidwa kwa akufa,+ iye adzafalitsa kuwala+ mwa anthu awa ndi kwa anthu a mitundu ina.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena