Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ Mateyu 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Mwana wa munthu+ akadzafika mu ulemerero wake, limodzi ndi angelo ake onse,+ adzakhala pampando wake wachifumu waulemerero.+ Chivumbulutso 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nditayang’ana, ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Limodzi naye panali enanso 144,000+ olembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pamphumi pawo.
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
31 “Mwana wa munthu+ akadzafika mu ulemerero wake, limodzi ndi angelo ake onse,+ adzakhala pampando wake wachifumu waulemerero.+
14 Nditayang’ana, ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Limodzi naye panali enanso 144,000+ olembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pamphumi pawo.