Chivumbulutso 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 57/1/1995, tsa. 1312/15/1988, tsa. 20 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 198-200
14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo.
14:1 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 57/1/1995, tsa. 1312/15/1988, tsa. 20 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 198-200