Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 1:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsiku lotsatira anaona Yesu akubwera kwa iye, ndipo anati: “Taonani, Mwanawankhosa+ wa Mulungu amene akuchotsa uchimo+ wa dziko!+

  • Chivumbulutso 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako ndinaona mwana wa nkhosa+ amene ankaoneka ngati waphedwa,+ ataimirira pakati pa mpando wachifumu ndi angelo 4 aja komanso pakati pa akulu aja.+ Iye anali ndi nyanga 7 ndiponso maso 7. Maso amenewa akuimira mizimu 7 ya Mulungu,+ imene yatumizidwa padziko lonse lapansi.

  • Chivumbulutso 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mulungu sadzatembereranso mzindawo. Koma mpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa+ udzakhala mumzindamo ndipo akapolo a Mulungu adzachita utumiki wopatulika kwa iye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena