Chivumbulutso 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.
21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.