Salimo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.” Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,* 1 Petulo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Paja Lemba limati: “Inetu ndikuika mwala wosankhidwa mwapadera mu Ziyoni. Umenewu ndi mwala wapakona ya maziko, womwe ndi wamtengo wapatali, ndipo aliyense wokhulupirira mwalawo sadzakhumudwa.”*+
6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”
22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,*
6 Paja Lemba limati: “Inetu ndikuika mwala wosankhidwa mwapadera mu Ziyoni. Umenewu ndi mwala wapakona ya maziko, womwe ndi wamtengo wapatali, ndipo aliyense wokhulupirira mwalawo sadzakhumudwa.”*+