Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 45:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mulungu ndi mpando wako wachifumu mpaka kalekale.+

      Ndodo ya ufumu wako ndi ndodo yachilungamo.+

  • Ezekieli 21:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ine ndidzawononga, ndidzawononga, ndidzawononga ufumu.* Ufumu umenewu sudzaperekedwa kwa wina aliyense mpaka atabwera amene ali woyenerera mwalamulo kuutenga,+ ndipo ndidzaupereka kwa iye.’+

  • Danieli 7:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndinapitiriza kuona masomphenya usikuwo ndipo ndinaona winawake wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera mʼmitambo. Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri+ uja ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Wamasiku Ambiriyo. 14 Kenako anamupatsa ulamuliro,+ ulemu+ ndi ufumu kuti anthu a mitundu yonse komanso anthu olankhula zilankhulo zosiyanasiyana azimutumikira.+ Ulamuliro wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo sudzatha. Ufumu wake sudzawonongedwa.+

  • Chivumbulutso 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pamalaya ake akunja komanso pantchafu yake, panalembedwa dzina lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena