Chivumbulutso 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo.
14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo.