Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 14:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Anthu inu mudzathawira kuchigwa chimene chidzakhale pakati pa mapiri anga,+ chifukwa chakuti chigwacho chidzafika mpaka ku Azeli. Mudzathawa ngati mmene munachitira pothawa chivomezi chimene chinachitika m’masiku a Uziya, mfumu ya Yuda.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanga adzabwera+ limodzi ndi oyera onse.+

  • Mateyu 13:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Mwana wa munthu adzatumiza angelo ake, ndipo adzachotsa mu ufumu wake zinthu zonse zopunthwitsa+ ndiponso anthu osamvera malamulo.

  • Mateyu 19:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Yesu anawayankha kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pa nthawi ya kulenganso zinthu, pamene Mwana wa munthu adzakhala pampando wachifumu waulemerero, inu amene mwatsatira ine mudzakhalanso m’mipando yachifumu 12, kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena