Deuteronomo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo anati:“Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+ Salimo 149:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuti awaweruze motsatira chigamulo cholembedwa.+Ulemerero umenewu ndi wa anthu onse okhulupirika a Mulungu.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Yoweli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu mitundu ya anthu yokhala mozungulira, bwerani mudzathandizane+ ndipo nonse musonkhane pamodzi.’”+ Inu Yehova, bweretsani ankhondo anu kumalo amenewo.+
2 Ndipo anati:“Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+
9 Kuti awaweruze motsatira chigamulo cholembedwa.+Ulemerero umenewu ndi wa anthu onse okhulupirika a Mulungu.+Tamandani Ya, anthu inu!+
11 Inu mitundu ya anthu yokhala mozungulira, bwerani mudzathandizane+ ndipo nonse musonkhane pamodzi.’”+ Inu Yehova, bweretsani ankhondo anu kumalo amenewo.+