Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+ Salimo 98:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+ Yuda 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhalenso Inoki,+ wa m’badwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova anabwera ndi miyandamiyanda ya oyera ake,*+
13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+
14 Ngakhalenso Inoki,+ wa m’badwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova anabwera ndi miyandamiyanda ya oyera ake,*+