Yesaya 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ineyo Yehova pochita zinthu mwachilungamo, ndinakuitana+ ndipo ndinakugwira dzanja.+ Ndidzakuteteza ndiponso ndidzakupereka monga pangano kwa anthu+ ngati kuwala kwa mitundu ya anthu,+
6 “Ineyo Yehova pochita zinthu mwachilungamo, ndinakuitana+ ndipo ndinakugwira dzanja.+ Ndidzakuteteza ndiponso ndidzakupereka monga pangano kwa anthu+ ngati kuwala kwa mitundu ya anthu,+