Luka 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.” Machitidwe 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano pamene iwo anamva zimenezi, anangovomereza,+ ndipo anatamanda Mulungu+ kuti: “Chabwino, pamenepa ndiye kuti Mulungu wapereka mwayi kwa anthu a mitundu ina kuti iwonso alape ndi kudzapeza moyo.”+ Machitidwe 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chotero dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzaimvetsera.”+ Aroma 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+
32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.”
18 Tsopano pamene iwo anamva zimenezi, anangovomereza,+ ndipo anatamanda Mulungu+ kuti: “Chabwino, pamenepa ndiye kuti Mulungu wapereka mwayi kwa anthu a mitundu ina kuti iwonso alape ndi kudzapeza moyo.”+
28 Chotero dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzaimvetsera.”+
9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+