Salimo 132:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+ Aroma 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso Yesaya anati: “Padzakhala muzu wa Jese,+ ndipo padzatuluka wina wodzalamulira mitundu.+ Mitundu idzayembekezera iye.”+ Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+
11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+
12 Komanso Yesaya anati: “Padzakhala muzu wa Jese,+ ndipo padzatuluka wina wodzalamulira mitundu.+ Mitundu idzayembekezera iye.”+
16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+