Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+

  • 1 Mbiri 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “‘“Masiku ako akadzakwana kuti ukakhale pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndithu ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako,+ imene idzakhala mmodzi wa ana ako, ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+

  • Luka 1:69
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 69 Iye watikwezera ife nyanga*+ yachipulumutso m’nyumba ya mtumiki wake Davide,

  • Machitidwe 13:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kuchokera mwa ana+ a munthu ameneyu, malinga ndi lonjezo lake, Mulungu wabweretsa mpulumutsi mu Isiraeli,+ amene ndi Yesu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena