1 Mafumu 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inenso ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu mu ufumu wa Isiraeli mpaka kalekale, monga momwe ndinalonjezera Davide bambo ako kuti, ‘Munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+ 1 Mbiri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli. Yeremiya 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “ndipo Davide ndidzamuutsira mphukira yolungama.+ Ndithudi mfumu idzalamulira+ m’dzikoli ndi kuchita zinthu mozindikira, motsatira malamulo komanso mwachilungamo.+
5 inenso ndidzakhazikitsa mpando wako wachifumu mu ufumu wa Isiraeli mpaka kalekale, monga momwe ndinalonjezera Davide bambo ako kuti, ‘Munthu wa m’banja lako sadzachoka pampando wachifumu wa Isiraeli.’+
5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.
5 “Taonani! Masiku adzafika,” watero Yehova, “ndipo Davide ndidzamuutsira mphukira yolungama.+ Ndithudi mfumu idzalamulira+ m’dzikoli ndi kuchita zinthu mozindikira, motsatira malamulo komanso mwachilungamo.+