1 Mafumu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova anakwaniritsa mawu amene ananena,+ kuti ineyo ndilowe m’malo mwa Davide bambo anga n’kukhala pampando wachifumu wa Isiraeli,+ monga momwe Yehova ananenera, ndiponso kuti ndimange nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Salimo 132:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+
20 Yehova anakwaniritsa mawu amene ananena,+ kuti ineyo ndilowe m’malo mwa Davide bambo anga n’kukhala pampando wachifumu wa Isiraeli,+ monga momwe Yehova ananenera, ndiponso kuti ndimange nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
11 Yehova walumbira kwa Davide,+Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+“Ndidzaika pampando wako wachifumu+Chipatso cha mimba yako.+