Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mulungu alange ine Abineri mowirikiza,+ ngati sindidzachitira Sauli mogwirizana ndi zimene Yehova analumbira kwa Davide,+

  • Salimo 89:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mulungu anati: “Ndachita pangano ndi wosankhidwa wanga.+

      Ndalumbira kwa Davide mtumiki wanga,+

  • Aheberi 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 (Pakuti pali amuna ena amene akhala ansembe popanda lumbiro, koma pali mmodzi amene wakhala wansembe mwa lumbiro. Lumbiro limeneli ndi la Iye amene ananena za wansembeyo kuti: “Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo) kuti, ‘Iwe ndiwe wansembe mpaka muyaya.’”)+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena