1 Mafumu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova wakwaniritsa zimene analonjeza, chifukwa ndalowa mʼmalo mwa bambo anga Davide ndipo ndakhala pampando wachifumu wa Isiraeli, mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza. Komanso ndamanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
20 Yehova wakwaniritsa zimene analonjeza, chifukwa ndalowa mʼmalo mwa bambo anga Davide ndipo ndakhala pampando wachifumu wa Isiraeli, mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza. Komanso ndamanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+