1 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+ 2 Mbiri 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova anakwaniritsa mawu+ amene ananena, kuti ineyo ndilowe m’malo mwa Davide bambo anga+ n’kukhala pampando wachifumu+ wa Isiraeli, monga momwe Yehova ananenera,+ ndiponso kuti ndimange nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+
10 Yehova anakwaniritsa mawu+ amene ananena, kuti ineyo ndilowe m’malo mwa Davide bambo anga+ n’kukhala pampando wachifumu+ wa Isiraeli, monga momwe Yehova ananenera,+ ndiponso kuti ndimange nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+