1 Mafumu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova anakwaniritsa mawu amene ananena,+ kuti ineyo ndilowe m’malo mwa Davide bambo anga n’kukhala pampando wachifumu wa Isiraeli,+ monga momwe Yehova ananenera, ndiponso kuti ndimange nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
20 Yehova anakwaniritsa mawu amene ananena,+ kuti ineyo ndilowe m’malo mwa Davide bambo anga n’kukhala pampando wachifumu wa Isiraeli,+ monga momwe Yehova ananenera, ndiponso kuti ndimange nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.+