Aroma 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwa njira imeneyi, Aisiraeli onse+ adzapulumuka. Izi zikugwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Wolanditsa adzachokera m’Ziyoni+ ndi kuchotsera Yakobo zochita zonse zosalemekeza Mulungu.+ Aroma 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kunena zoona,+ Khristu anakhaladi mtumiki+ kwa anthu odulidwa+ kuti atsimikizire kuti Mulungu ndi wokhulupirika. Komanso iye anasonyeza kuti malonjezo+ amene Mulunguyo anapatsa makolo awo ndi otsimikizirika,
26 Mwa njira imeneyi, Aisiraeli onse+ adzapulumuka. Izi zikugwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Wolanditsa adzachokera m’Ziyoni+ ndi kuchotsera Yakobo zochita zonse zosalemekeza Mulungu.+
8 Kunena zoona,+ Khristu anakhaladi mtumiki+ kwa anthu odulidwa+ kuti atsimikizire kuti Mulungu ndi wokhulupirika. Komanso iye anasonyeza kuti malonjezo+ amene Mulunguyo anapatsa makolo awo ndi otsimikizirika,