Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+

      Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+

  • Yesaya 29:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chotero Yehova, amene anawombola Abulahamu, wanena izi kwa nyumba ya Yakobo:+ “Tsopano Yakobo sachita manyazi. Tsopano nkhope yake sikhala yakugwa,+

  • Yoweli 2:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pamenepo mudzadya ndi kukhuta+ ndipo mudzatamanda dzina la Yehova Mulungu wanu+ amene wakuchitirani zodabwitsa.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena