Salimo 69:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Onse amene akuyembekezera inu asachite manyazi chifukwa cha ine,+Inu Ambuye Wamkulu Koposa, Yehova wa makamu.+Onse amene akufunafuna inu, asanyazitsidwe chifukwa cha ine,+Inu Mulungu wa Isiraeli.+
6 Onse amene akuyembekezera inu asachite manyazi chifukwa cha ine,+Inu Ambuye Wamkulu Koposa, Yehova wa makamu.+Onse amene akufunafuna inu, asanyazitsidwe chifukwa cha ine,+Inu Mulungu wa Isiraeli.+