Salimo 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+ Salimo 35:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+
3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+
26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+