Salimo 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi yatsoka sadzachita manyazi,+Ndipo pa nthawi ya njala adzakhuta.+ Zefaniya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku limenelo, sudzachita manyazi chifukwa cha zochita zako zimene unandilakwira nazo,+ pakuti ndidzachotsa pamaso pako anthu odzikweza amene amakhala mosangalala+ ndipo sudzakhalanso wodzikweza m’phiri langa lopatulika.+ Aroma 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndipo chiyembekezocho sichitikhumudwitsa+ chifukwa Mulungu wadzaza chikondi chake+ m’mitima yathu+ kudzera mwa mzimu woyera+ umene tinapatsidwa.
11 Pa tsiku limenelo, sudzachita manyazi chifukwa cha zochita zako zimene unandilakwira nazo,+ pakuti ndidzachotsa pamaso pako anthu odzikweza amene amakhala mosangalala+ ndipo sudzakhalanso wodzikweza m’phiri langa lopatulika.+
5 ndipo chiyembekezocho sichitikhumudwitsa+ chifukwa Mulungu wadzaza chikondi chake+ m’mitima yathu+ kudzera mwa mzimu woyera+ umene tinapatsidwa.