1 Yohane 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma aliyense wosunga mawu ake,+ amasonyeza kuti amakondadi Mulungu.+ Chifukwa cha zimenezi, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+ 2 Yohane 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo chikondi chimenechi chimatanthauza kuti+ tiziyendabe motsatira malamulo ake.+ Monga mmene munamvera kuyambira pachiyambi, lamulo lake ndi lakuti mupitirize kuyenda m’chikondi,+
5 Koma aliyense wosunga mawu ake,+ amasonyeza kuti amakondadi Mulungu.+ Chifukwa cha zimenezi, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+
6 Ndipo chikondi chimenechi chimatanthauza kuti+ tiziyendabe motsatira malamulo ake.+ Monga mmene munamvera kuyambira pachiyambi, lamulo lake ndi lakuti mupitirize kuyenda m’chikondi,+