1 Yohane 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’chikondi mulibe mantha,+ koma chikondi chimene chili chokwanira chimathetsa mantha,+ chifukwa mantha amachititsa munthu kukhala womangika. Amene ali ndi mantha, chikondi chake si chokwanira.+
18 M’chikondi mulibe mantha,+ koma chikondi chimene chili chokwanira chimathetsa mantha,+ chifukwa mantha amachititsa munthu kukhala womangika. Amene ali ndi mantha, chikondi chake si chokwanira.+