Yohane 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa tsikulo mudzadziwa kuti ine ndili wogwirizana ndi Atate, inunso ndi ine ndife ogwirizana.+ Yohane 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kuti onsewa akhale amodzi,+ mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife,+ ndi kuti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.+
21 kuti onsewa akhale amodzi,+ mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife,+ ndi kuti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.+