2 Akorinto 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye watiikanso chidindo+ chake chotitsimikizira ndipo watipatsa m’mitima mwathu chikole+ cha madalitso am’tsogolo, ndicho mzimu.+ Agalatiya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano pakuti ndinu ana ake, Mulunguyo watitumizira mzimu+ wa Mwana wake m’mitima yathu ndipo mzimuwo ukufuula kuti: “Abba,* Atate!”+
22 Iye watiikanso chidindo+ chake chotitsimikizira ndipo watipatsa m’mitima mwathu chikole+ cha madalitso am’tsogolo, ndicho mzimu.+
6 Tsopano pakuti ndinu ana ake, Mulunguyo watitumizira mzimu+ wa Mwana wake m’mitima yathu ndipo mzimuwo ukufuula kuti: “Abba,* Atate!”+