Yohane 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+ Aroma 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndipo chiyembekezocho sichitikhumudwitsa+ chifukwa Mulungu wadzaza chikondi chake+ m’mitima yathu+ kudzera mwa mzimu woyera+ umene tinapatsidwa.
26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+
5 ndipo chiyembekezocho sichitikhumudwitsa+ chifukwa Mulungu wadzaza chikondi chake+ m’mitima yathu+ kudzera mwa mzimu woyera+ umene tinapatsidwa.