Yoweli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndili pakati pa Isiraeli,+ ndiponso kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu ndipo palibenso Mulungu wina.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.
27 Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndili pakati pa Isiraeli,+ ndiponso kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu ndipo palibenso Mulungu wina.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.